Mateyu 25:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chifukwa ndinamva njala koma inu munandipatsa chakudya. Ndinamva ludzu koma inu munandipatsa chakumwa. Ndinali mlendo koma inu munandilandira bwino.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:35 Nsanja ya Olonda,10/15/1995, ptsa. 25-26
35 Chifukwa ndinamva njala koma inu munandipatsa chakudya. Ndinamva ludzu koma inu munandipatsa chakumwa. Ndinali mlendo koma inu munandilandira bwino.+