Mateyu 25:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndinali wamaliseche* koma inu munandiveka.+ Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali mʼndende koma inu munabwera kudzandiona.’+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:36 Nsanja ya Olonda,10/15/1995, ptsa. 25-26
36 Ndinali wamaliseche* koma inu munandiveka.+ Ndinadwala koma inu munandisamalira. Ndinali mʼndende koma inu munabwera kudzandiona.’+