-
Mateyu 25:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Iwonso adzayankha kuti: ‘Ambuye, tinakuonani liti muli ndi njala kapena muli ndi ludzu kapena muli mlendo kapena muli wamaliseche kapena mukudwala kapena muli mʼndende ife osakutumikirani?’
-