Mateyu 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zimene mayiyu wachita pothira mafuta onunkhirawa pathupi langa, wazichita pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+
12 Zimene mayiyu wachita pothira mafuta onunkhirawa pathupi langa, wazichita pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+