-
Mateyu 26:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Choncho ophunzirawo anachitadi mogwirizana ndi zimene Yesu anawauza ndipo anakonza zinthu zonse zofunika pa Pasika.
-