Mateyu 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yamadzulo,+ iye ndi ophunzira ake 12 aja anakhala patebulo nʼkumadya chakudya.+