-
Mateyu 26:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Yudasi amene anali atatsala pangʼono kumupereka anayankha kuti: “Nanga nʼkukhala ine Rabi?” Yesu anamuyankha kuti: “Wanena wekha.”
-