Mateyu 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anamuuza kuti: “Ndithudi ndikukuuza iwe, usiku womwe uno tambala asanalire, undikana katatu.”+
34 Yesu anamuuza kuti: “Ndithudi ndikukuuza iwe, usiku womwe uno tambala asanalire, undikana katatu.”+