Mateyu 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako Yesu anafika nawo pamalo otchedwa Getsemane,+ ndipo anauza ophunzirawo kuti: “Khalani pansi panopa, ine ndikupita uko kukapemphera.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:36 Yesu—Ndi Njira, tsa. 282 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 8
36 Kenako Yesu anafika nawo pamalo otchedwa Getsemane,+ ndipo anauza ophunzirawo kuti: “Khalani pansi panopa, ine ndikupita uko kukapemphera.”+