Mateyu 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Popita kumeneko anatenga Petulo ndi ana awiri a Zebedayo. Ndipo anayamba kumva chisoni komanso kuvutika kwambiri mumtima mwake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:37 Yesu—Ndi Njira, tsa. 282 Nsanja ya Olonda,5/15/1996, tsa. 21
37 Popita kumeneko anatenga Petulo ndi ana awiri a Zebedayo. Ndipo anayamba kumva chisoni komanso kuvutika kwambiri mumtima mwake.+