Mateyu 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atatero anabwerera pamene panali ophunzira ake aja ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Zoona simungathe kukhalabe maso limodzi ndi ine kwa ola limodzi?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:40 Nsanja ya Olonda,1/1/2003, tsa. 205/15/1996, tsa. 21
40 Atatero anabwerera pamene panali ophunzira ake aja ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Zoona simungathe kukhalabe maso limodzi ndi ine kwa ola limodzi?+