Mateyu 26:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Yesu anamufunsa kuti: “Bwanawe, wabwera kudzatani kuno?”+ Nthawi yomweyo iwo anayandikira ndipo anagwira Yesu nʼkumumanga. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:50 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284
50 Koma Yesu anamufunsa kuti: “Bwanawe, wabwera kudzatani kuno?”+ Nthawi yomweyo iwo anayandikira ndipo anagwira Yesu nʼkumumanga.