Mateyu 26:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Mu ola lomwelo Yesu anafunsa gulu la anthulo kuti: “Bwanji mwabwera kudzandigwira mutatenga malupanga ndi zibonga ngati mukudzalimbana ndi wachifwamba? Tsiku ndi tsiku ndinkakhala pansi mʼkachisi nʼkumaphunzitsa,+ koma simunandigwire.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:55 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2020, tsa. 31
55 Mu ola lomwelo Yesu anafunsa gulu la anthulo kuti: “Bwanji mwabwera kudzandigwira mutatenga malupanga ndi zibonga ngati mukudzalimbana ndi wachifwamba? Tsiku ndi tsiku ndinkakhala pansi mʼkachisi nʼkumaphunzitsa,+ koma simunandigwire.+