Mateyu 26:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Koma Petulo anapitiriza kumutsatira ali chapatali ndithu, mpaka anafika mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembeyo. Atalowa mkati, anakhala pansi limodzi ndi antchito amʼnyumbamo kuti aone zotsatira zake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:58 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, ptsa. 199-200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, ptsa. 22-2311/15/1990, tsa. 8
58 Koma Petulo anapitiriza kumutsatira ali chapatali ndithu, mpaka anafika mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembeyo. Atalowa mkati, anakhala pansi limodzi ndi antchito amʼnyumbamo kuti aone zotsatira zake.+
26:58 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, ptsa. 199-200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, ptsa. 22-2311/15/1990, tsa. 8