Mateyu 26:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Ndiyeno ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* ankafunafuna umboni wabodza kuti anamizire Yesu mlandu nʼcholinga choti amuphe.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:59 Nsanja ya Olonda,4/1/2011, tsa. 19
59 Ndiyeno ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* ankafunafuna umboni wabodza kuti anamizire Yesu mlandu nʼcholinga choti amuphe.+