Mateyu 26:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Yesu anamuyankha kuti: “Mwanena nokha. Koma ndikukuuzani kuti: Kuyambira panopa mpaka mʼtsogolo mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja lamphamvu.+ Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:64 Yesu—Ndi Njira, tsa. 287 Nsanja ya Olonda,6/1/2011, tsa. 1811/1/1990, tsa. 91/1/1988, ptsa. 10-11
64 Yesu anamuyankha kuti: “Mwanena nokha. Koma ndikukuuzani kuti: Kuyambira panopa mpaka mʼtsogolo mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja lamphamvu.+ Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+
26:64 Yesu—Ndi Njira, tsa. 287 Nsanja ya Olonda,6/1/2011, tsa. 1811/1/1990, tsa. 91/1/1988, ptsa. 10-11