Mateyu 26:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Tsopano Petulo anali atakhala pansi mʼbwalolo ndipo mtsikana wina wantchito anabwera kwa iye nʼkunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu wa ku Galileyayu!”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:69 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
69 Tsopano Petulo anali atakhala pansi mʼbwalolo ndipo mtsikana wina wantchito anabwera kwa iye nʼkunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu wa ku Galileyayu!”+