Mateyu 26:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Atatuluka nʼkupita pakanyumba kapageti, mtsikana winanso anamuzindikira nʼkuuza ena amene anali pafupi kuti: “Bambo awa anali limodzi ndi Yesu Mnazaretiyu.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:71 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
71 Atatuluka nʼkupita pakanyumba kapageti, mtsikana winanso anamuzindikira nʼkuuza ena amene anali pafupi kuti: “Bambo awa anali limodzi ndi Yesu Mnazaretiyu.”+