-
Mateyu 26:73Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
73 Patapita kanthawi pangʼono, amene anali ataimirira chapafupi anabwera nʼkuuza Petulo kuti: “Ndithu iwenso uli mʼgulu la ophunzira ake ndipo kalankhulidwe kako kakugwiritsa.”
-