-
Mateyu 26:74Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
74 Pamenepo iye anayamba kutemberera ndi kulumbira kuti: “Munthu ameneyu ine sindikumudziwa ayi!” Nthawi yomweyo tambala analira.
-