Mateyu 26:75 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 Ndiyeno Petulo anakumbukira mawu a Yesu aja akuti: “Tambala asanalire, udzandikana katatu.”+ Ndipo anatuluka panja nʼkuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:75 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, ptsa. 8-9
75 Ndiyeno Petulo anakumbukira mawu a Yesu aja akuti: “Tambala asanalire, udzandikana katatu.”+ Ndipo anatuluka panja nʼkuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri.