Mateyu 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yudasi amene anamupereka uja, ataona kuti Yesu waweruzidwa kuti aphedwe, anavutika koopsa mumtima moti anapita kukabweza ndalama 30 zasiliva zija kwa ansembe aakulu ndiponso akulu.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:3 Nsanja ya Olonda,1/15/2008, tsa. 31
3 Kenako Yudasi amene anamupereka uja, ataona kuti Yesu waweruzidwa kuti aphedwe, anavutika koopsa mumtima moti anapita kukabweza ndalama 30 zasiliva zija kwa ansembe aakulu ndiponso akulu.+