-
Mateyu 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma ansembe aakulu anatenga ndalama zasilivazo nʼkunena kuti: “Nʼzosaloleka kuti ndalamazi ziikidwe mʼmalo opatulika osungiramo chuma, chifukwa ndi malipiro a magazi.”
-