Mateyu 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo anagulira munda wa woumba mbiya, mogwirizana ndi zimene Yehova* anandilamula.”+