-
Mateyu 27:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho anthu atasonkhana pamodzi, Pilato ananena kuti: “Kodi mukufuna kuti ndikumasulireni ndani, Baraba kapena Yesu amene mumati ndi Khristu?”
-