Mateyu 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ koma kuti Yesu aphedwe.+
20 Komabe ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ koma kuti Yesu aphedwe.+