Mateyu 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, amene mumati ndi Khristu uja, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”*+
22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, amene mumati ndi Khristu uja, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”*+