Mateyu 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anati: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma anthuwo anapitiriza kufuula mwamphamvu kuti: “Ameneyo apachikidwe basi!”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:23 Yesu—Ndi Njira, tsa. 294
23 Iye anati: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma anthuwo anapitiriza kufuula mwamphamvu kuti: “Ameneyo apachikidwe basi!”+