-
Mateyu 27:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ataona kuti sizikuthandiza komanso kuti pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi nʼkusamba mʼmanja pamaso pa gulu la anthulo ndipo ananena kuti: “Ine ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.”
-