Mateyu 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho anawamasulira Baraba, koma analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:26 Yesu—Ndi Njira, tsa. 294 Nsanja ya Olonda,1/1/1991, tsa. 9 Mawu a Mulungu, tsa. 61
26 Choncho anawamasulira Baraba, koma analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+