Mateyu 27:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero anamulavulira+ ndipo anatenga bango lija nʼkuyamba kumumenya nalo mʼmutu. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:30 “Wotsatira Wanga,” tsa. 174