Mateyu 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atamaliza kumunyozako, anamuvula chinsalu chija nʼkumuveka malaya ake akunja ndipo anapita naye kuti akamukhomerere pamtengo.+
31 Atamaliza kumunyozako, anamuvula chinsalu chija nʼkumuveka malaya ake akunja ndipo anapita naye kuti akamukhomerere pamtengo.+