Mateyu 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ali mʼnjira, anakumana ndi munthu wina wa ku Kurene, dzina lake Simoni. Iwo anakakamiza munthu ameneyu kuti asenze mtengo wozunzikirapo* wa Yesu.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:32 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 296-297 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 6
32 Ali mʼnjira, anakumana ndi munthu wina wa ku Kurene, dzina lake Simoni. Iwo anakakamiza munthu ameneyu kuti asenze mtengo wozunzikirapo* wa Yesu.+