Mateyu 27:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno achifwamba awiri anapachikidwa naye limodzi. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja ndipo wina anali kumanzere kwake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:38 Nsanja ya Olonda,2/1/2012, tsa. 148/15/2011, tsa. 1410/1/2008, ptsa. 5-6
38 Ndiyeno achifwamba awiri anapachikidwa naye limodzi. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja ndipo wina anali kumanzere kwake.+