Mateyu 27:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 nʼkumanena kuti: “Iwe amene unkanena kuti ungathe kugwetsa kachisi nʼkumumanga mʼmasiku atatu,+ dzipulumutse! Ngati ulidi mwana wa Mulungu, tsikatu pamtengo wozunzikirapowo!”*+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:40 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
40 nʼkumanena kuti: “Iwe amene unkanena kuti ungathe kugwetsa kachisi nʼkumumanga mʼmasiku atatu,+ dzipulumutse! Ngati ulidi mwana wa Mulungu, tsikatu pamtengo wozunzikirapowo!”*+