Mateyu 27:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Chimodzimodzinso ansembe aakulu limodzi ndi alembi komanso akulu. Nawonso anayamba kumunyoza nʼkumanena kuti:+
41 Chimodzimodzinso ansembe aakulu limodzi ndi alembi komanso akulu. Nawonso anayamba kumunyoza nʼkumanena kuti:+