Mateyu 27:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga siponji nʼkuiviika muvinyo wowawasa ndipo anaiika kubango nʼkumupatsa kuti amwe.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:48 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 15
48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga siponji nʼkuiviika muvinyo wowawasa ndipo anaiika kubango nʼkumupatsa kuti amwe.+