Mateyu 27:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Tsopano madzulo kwambiri, kunabwera munthu wina wachuma wa ku Arimateya, dzina lake Yosefe, amenenso anakhala wophunzira wa Yesu.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:57 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 1610/1/2008, ptsa. 5-6
57 Tsopano madzulo kwambiri, kunabwera munthu wina wachuma wa ku Arimateya, dzina lake Yosefe, amenenso anakhala wophunzira wa Yesu.+