Mateyu 27:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Iye anapita kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu+ ndipo Pilato analamula kuti amupatse mtembowo.+