Mateyu 27:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya wina anatsalira komweko, atakhala pansi pafupi ndi mandawo.+
61 Koma Mariya wa ku Magadala ndi Mariya wina anatsalira komweko, atakhala pansi pafupi ndi mandawo.+