Mateyu 27:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 nʼkunena kuti: “Bwana, ife takumbukira kuti munthu wachinyengo uja adakali moyo ananena kuti, ‘Pakadzadutsa masiku atatu ndidzaukitsidwa.’+
63 nʼkunena kuti: “Bwana, ife takumbukira kuti munthu wachinyengo uja adakali moyo ananena kuti, ‘Pakadzadutsa masiku atatu ndidzaukitsidwa.’+