Mateyu 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mngeloyo ankaoneka ngati mphezi ndipo zovala zake zinali zoyera kwambiri.+