Mateyu 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muno mulibe chifukwa waukitsidwa mogwirizana ndi zimene ananena.+ Bwerani muone pamene anagona.