Mateyu 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti waukitsidwa kwa akufa, moti panopa watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2020, ptsa. 2-3
7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti waukitsidwa kwa akufa, moti panopa watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+