-
Mateyu 28:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako Yesu anawauza kuti: “Musaope! Pitani mukauze abale anga kuti apite ku Galileya ndipo akandiona kumeneko.”
-