-
Mateyu 28:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho anatenga ndalama zasilivazo nʼkuchita mogwirizana ndi zimene anawauza ndipo nkhani imeneyi ndi yofala kwambiri pakati pa Ayuda mpaka lero.
-