Maliko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho anthu onse amene ankakhala mʼdera la Yudeya komanso onse amene ankakhala mu Yerusalemu ankapita kwa iye. Yohane ankawabatiza* mumtsinje wa Yorodano ndipo anthuwo ankaulula machimo awo poyera.+
5 Choncho anthu onse amene ankakhala mʼdera la Yudeya komanso onse amene ankakhala mu Yerusalemu ankapita kwa iye. Yohane ankawabatiza* mumtsinje wa Yorodano ndipo anthuwo ankaulula machimo awo poyera.+