Maliko 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yohane ankavala chovala chaubweya wa ngamila ndi lamba wachikopa mʼchiuno mwake+ ndipo ankadya dzombe ndi uchi.+
6 Yohane ankavala chovala chaubweya wa ngamila ndi lamba wachikopa mʼchiuno mwake+ ndipo ankadya dzombe ndi uchi.+