Maliko 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye ankalalikira kuti: “Pambuyo pangapa pakubwera winawake wamphamvu kuposa ine amene sindili woyenera kuwerama nʼkumasula zingwe za nsapato zake.+
7 Iye ankalalikira kuti: “Pambuyo pangapa pakubwera winawake wamphamvu kuposa ine amene sindili woyenera kuwerama nʼkumasula zingwe za nsapato zake.+