Maliko 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho iye anakhala mʼchipululumo masiku 40, akuyesedwa ndi Satana.+ Mʼchipululumo munalinso nyama zakutchire ndipo angelo ankamutumikira.+
13 Choncho iye anakhala mʼchipululumo masiku 40, akuyesedwa ndi Satana.+ Mʼchipululumo munalinso nyama zakutchire ndipo angelo ankamutumikira.+